Tsoka Liyenda lyrics by Langwan Piksy - original song full text. Official Tsoka Liyenda lyrics, 2024 version | LyricsMode.com
Request & respond explanations
  • Don't understand the meaning of the song?
  • Highlight lyrics and request an explanation.
  • Click on highlighted lyrics to explain.
Langwan Piksy – Tsoka Liyenda lyrics
Kumbire adanka nawo
Palibe akanakhonza
Anasiya pa dzuwa anawo
Anayesa ndi malodza
Ankati satana
Wakhala pa nsana
Kuyamba kudana
Kufuna kuphana
Kuthana
Nzosauzana
Nthawi yakwana
Buluzi wa easy chitseko cha mpana

Chorus
Anapita ndi nyanga zomwe kumanda
Anapita ndi nyanga zomwe kumanda
Ayo
Tsoka Liyenda
Ayo
Tsoka Liyenda

Bambo awa anali chikhwaya
Ana moyo wawo sanamve kuwawa
Ku school akapita amathawa
Zinavuta ndi za nchere analawa
Yes
Sanauzidwe za moyo
Anapeza bwanji makolo
Chuma
Moyo unakoma
Opanda zo khoma
Kupeza izo afuna
Ohh dzi ana ulesi
Bambo awo atsamira nkono

Akuti zonsezi
Ndi curse
Chayabwa chitedze
Mavuto pang'ono see they stressed
Chorus
Anapita ndi nyanga zomwe kumanda
Anapita ndi nyanga zomwe kumanda
Ayo
Tsoka Liyenda
Ayo
Tsoka Liyenda

Mudziwaphunzitsa ana
Skupangira pa mawa
Asamayese ngati ophweka moyo
Mukadzapita adzakhala akapolo

Musama yiwale
Kuti zanu munapanga kale
Nzeru zanu sizingatsale
Mungadzavutitse abale
Mdzakolola zomwe mudzale
Chuma ichi sangasamale
Ngati panopa simuphunzitsa
Mapangidwe ake mukumpusitsa
Tsoka ilo
Chorus
Anapita ndi nyanga zomwe kumanda
Anapita ndi nyanga zomwe kumanda
Ayo
Tsoka Liyenda
Ayo
Tsoka Liyenda
×



Lyrics taken from /lyrics/l/langwan_piksy/tsoka_liyenda.html

  • Email
  • Correct
Submitted by Langwan_Piksy

Tsoka Liyenda meanings

Write about your feelings and thoughts about Tsoka Liyenda

Know what this song is about? Does it mean anything special hidden between the lines to you? Share your meaning with community, make it interesting and valuable. Make sure you've read our simple tips.
U
Min 50 words
Not bad
Good
Awesome!

Post meanings

U
Min 50 words
Not bad
Good
Awesome!

official video

Featured lyrics

0-9 A B C D E F G H I J K L M N O P Q R S T U V W X Y Z